
Gulu La Malawi National Dance Troupe Likayimba Ku Japan
Gulu la Malawi National Dance Troupe likuyembekezeka kukayimba m’dziko la Japan pa mwambo wa Japan World Expo 2025 mwezi uno wa June. Gululi lati ndilokondwa ndi losangalala chifukwa chopeza mwayi ngati umenewu okayimba m’dziko la Japan. M’modzi wa gululi, James…









