Ndizotheka Kuteteza Chilengedwe Ndi Zinyalala

Potsatira maphunziro, omwe anali nawo mwezi wa May okhudza kapangidwe kamakala ochokera kuzinyalala, achinyamata a gulu la Kafoteka mu boma la Mzimba ayamba kupanga paokha makalawa. Guliri, lomwe limachokera m’mudzi mwa Inkosi Mmbelwa, lati atachita maphunziro wa kwatsiku limodzi anaona…




