
TIMU YA MPIRA WA MANJA YA SENA MODELS YA KU NSANJE AYIYAMIKIRA
Timu ya mpira wa manja ya Sena Models ndi yokhayo yomwe idayamba kusewera kalekale m’boma la Nsanje. Peter Mizedya yemwe ndi m’phunzitsi wa timuyi wati, timuyi idayambitsidwa kaamba ka kolowerera kwa atsikanawa. Iwo ati mudali mu chaka cha 2012 pomwe…









