
Gulu la Amai A Sarah Achezera Odwala Pa Chipatala Cha Kalemba
Gulu la amai la Sara mu mpingo wa Living Waters International, nthambi ya pa Bangula adachezera wodwala pa chipatala cha Kalemba mu nyengo ya chikondwerero cha Khisimisi. Mai Mbusa Priscilla M’bwana ati adachiwona choyenera kukachereza odwala omwe sakadatha kukhala ndi…









