KUSAMALA IPHUNZITSA ATOLANKHANI ULIMI WA MAKOLO
Bungwe la Kusamala Institute of Agriculture and Ecology lalimbikitsa atolankhani m’dziko kugawa uthenga olimbikitsa ulimi ogwiritsa ntchito mbeu komaso njira zamakolo uja pa chingerezi amati organic. Iwo anena izi pa mkumano omwe anakonza ku Lilongwe ndipo mkumanowu unabweretsa pamodzi atolankhani…