MKULU WA APOLISI KU CHIKWAWA AMEMA AMAYI KULEWA NKHANZA
Mkulu wa a polisi m’boma la Chikwawa Assistant Commissioner of Police (ACP) Carolyn Jere amema amayi kuti akhale a chikondi poonetsa mtima wa chikondi waunakubala popewa nkhanza za mtundu uliwonse. A Jere ati apolisi a akazi kwa masiku atatu akhala…