
BUNGWE LA CARD ALIPEMPHA KUTI LIFALITSE UTHENGA WAUCHEMBERE WABWINO
Bungwe la Churches Action in Relief and Development (CARD) alipempha kuti lifikire madera ena omwe ngovuta kufikilika ndi uthenga wuchimbere wabwino. Izi zithandiza kupewa kutenga mimba pakati pa atsikana achichepere. Nyakwawa Yayikulu Kanyimbi ya m’dera la Mfumu Yayikulu Tengani m’boma…





