
MAYI WAMALONDA AKWANITSA KUTUKUKA KUDZELA MU MALONDA OGULITSA TIYI
Mayi Elifa Letiya aku Mitundu m’boma la Lilongwe ndi chitsanzo chabwino pakati pa amayi anzawo atakwanitsa kusintha moyo wawo pankhani za chuma kudzera mu malonda ogulitsa tiyi. Kwa nthawi yaitali, Mayi Letiya akhala akuchita malonda ogulitsa tiyi komanso ma sikono…