MDAUKU WA TONGA UCHITIKA MU AUGUST
Akuluakulu omwe akuyendetsa zokonzekera zokhudza mwambo wa chikhalidwe cha a Tonga omwe umadziwika kuti Mdauku wa Tonga ati zokonzekera zili m’chimake kuti mwambowu uchitike m’mwezi wa August. M’modzi mwa akuluakulu omwe akuyendetsa zokonzekera za mwambowu Goodwin Njikho wauza ProjectM kuti…