
RODWELL LUMBE APITILIZA KUFIKIRA ANTHU A ULUMALI
Wachinyamata yemwe amadziwika ndi ntchito zachifundo mdziko muno Rodwell Lumbe wati mwambo wa Christmas luncheon uliko chaka chino. Uwu ndi mwambo omwe umachitika chaka ndi chaka omwe ati cholinga chake ndikufuna kufikira anthu amaulumali osiyanasiyana pokwendwelera chikondwelero cha Christmas. Polemba…