Thokozani Mnolo

Thokozani Mnolo

Achinyamata Aku Mzimba Ayamba Kuteteza Chilengedwe

M’modzi mwa achinyamata omwe akugwira ntchito yofuna kuteteza chilengedwe m’boma la Mzimba Anthony Botha wayamba ntchito yophunzitsa achinyamata kapangidwe kamakala otchedwa ‘briquettes’ m’chingereezi. Botha yemwe akugwira ntchitoyi mongodzipereka wati anachiona chanzeru kuphunzitsa achinyamatawa potengera kuti achinyamata ali ndi udindo waukulu…