NTCHITO YOMANGA SUKULU YA MPATSA PULAYIMALE IYAMBA POSACHEDWA

Mkulu wa bungwe loona za mavuto odza mwadzidzi m’dziko muno la Department of Disaster and Management Affairs (DoDMA), Commissioner Charles Kalemba atsimikizira anthu a m’dera la Mfumu Yayikulu Tengani m’boma la Nsanje kuti ntchito yomanga sukulu ya pulayimale ya Mpatsa…